
Henry Czar – Million (Official Music Video)
Directed by Keong Kadango
VFX effects by Matt The Creator
https://www.facebook.com/henryczarmw
https://www.instagram.com/henryczar.mw/
https://x.com/HenryCzarmw
Get audio here
https://linktr.ee/henryczar_Million
This song was inspired by the legendary Ian LIzi
Produced by Mingo & Dj Brown
Written & composed by Henry Czar
Lyrics
Ndimafuna nditagula mansion
Ngati bwa kusitha Lamborghini
Dollar kudzadzitsa mkatoni
Homie akamwe jambogin
Ofcoz will always be humble
adah Chimfana cha Low-key
Kupeza dollar zambiri mkumakonda beans ungathe kuphura sin
Mtafika level ya Simbi Simbi
Simbi angathe kusimba Simba
Koma kamfana koyimba Kaja
Kali makola sikali lamba
Ekhaya ekhaya
Mpinganjila kudzandikhola
Mwatchinga njira afana tidutseko tikudziwa mwayiphula
Mandede!
Ndede ndede ma five handede
(Million million)
Mandede!
Ndede ndede ma five handede
(Million million)
Ndimafuna nditapeza handede
(Million)
Olo five handede
(Million)
Level ya mpinganjira
(Billionaire)
Yehovah kutsekula njira
(Billion Billion)
Atate! Ambuye!
Mundiyakhe pephero langa
Mundipatse zosowa zanga
Munditsogolele
Ndikamakhala ndimazadziwa kuti day inayake dzayiphula
Ndikangogwadwa ndimamupepha kuti makomo atsegula
Ndimayesetsa kulimbikila kuti uphawi uthepo
Kuti chuma chisefukile uphawi ukhawulepo
Mandede!
Ndede ndede ma five handede
(Million million)
Mandede!
Ndede ndede ma five handede
(Million million)
Ndimafuna nditapeza handede
(Million)
Olo five handede
(Million)
Level ya mpinganjira
(Billionaire)
Yehovah kutsekula njira
(Billion Billion)
Comment ×